Genesis 29:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adaŵafunsa abusawo kuti, “Kodi abale anga mukuchokera kuti?” Iwowo adayankha kuti, “Tikuchokera ku Harani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati Yakobo kwa iwo, Abale anga, ndinu a kuti inu? Nati, Ndife a ku Harani.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anafunsa abusawo kuti, “Abale anga, mwachokera kuti?” Iwo anayankha, “Tachokera ku Harani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati Yakobo kwa iwo, Abale anga, ndinu a kuti inu? nati, Ndife a ku Harana.