Genesis 29:5 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adafunsanso kuti, “Kodi Labani mwana wa Nahori mumamdziŵa?” Iwowo adayankha kuti, “Ee, timamdziŵa.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anati kwa iwo, Kodi mumdziwa Labani mwana wake wa Nahori? Nati, Timdziwa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anawafunsanso kuti, “Kodi Labani, mdzukulu wa Nahori mukumudziwa?” Iwo anayankha, “Inde tikumudziwa?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anati kwa iwo, Kodi mumdziwa Labani mwana wace wa Nahori? nati, Timdziwa.