Genesis 3:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamu adatcha mkazi wake Heva, chifukwa choti iyeyu anali mai wa anthu onse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo mwamuna anamutcha dzina la mkazi wake, Heva; chifukwa ndiye amake wa amoyo onse.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Munthu uja anatcha mkazi wake Hava, chifukwa iyeyu adzakhala mayi wa anthu onse amoyo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo mwamuna anamucha dzina la mkazi wace, Hava; cifukwa ndiye amace wa amoyo onse.