Genesis 30:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo Zilipa adabala mwana wamwamuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Zilipa mdzakazi wake wa Leya anambalira Yakobo mwana wamwamuna.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zilipa, wantchito wa Leya, anaberekera Yakobo mwana wamwamuna.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Zilipa mdzakazi wace wa Leya anambalira Yakobo mwana wamwamuna.