Genesis 30:12 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Zilipa mdzakazi wa Leyayo adamubaliranso Yakobe mwana wamwamuna wachiŵiri.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Zilipa mdzakazi wa Leya anambalira Yakobo mwana wamwamuna wachiwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Zilipa, wantchito wa Leya anamubalira Yakobo mwana wa mwamuna wachiwiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Zilipa mdzakazi wa Leya anambalira Yakobo mwana wamwamuna waciwiri.