Genesis 30:21 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pambuyo pake adabala mwana wamkazi, namutcha Dina.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pambuyo pake ndipo anabala mwana wamkazi, namutcha dzina lake Dina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita nthawi Leya anabereka mwana wamkazi ndipo anamutcha Dina.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pambuyo pace ndipo anabala mwana wamkazi, namucha dzina lace Dina.