Genesis 30:22 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Mulungu adakumbukira Rakele, namva pemphero lake, nkulola kuti abale ana.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mulungu anakumbukira Rakele, ndipo Mulungu anamvera iye, natsegula m'mimba mwake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kenaka, Mulungu anakumbukira Rakele namva pemphero lake ndi kulola kuti akhale ndi mwana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mulungu anakumbukila Rakele, ndipo Mulungu anamvera iye, natsegula m'mimba mwace.