Genesis 30:24 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero mwanayo adamutcha Yosefe, nanena kuti, “Mulungu andipatse wina mwana.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
namutcha dzina lake Yosefe; ndipo anati, Yehova anandionjezera ine mwana wamwamuna wina.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Iye anamutcha mwanayo Yosefe, ndipo anati, “Mulungu andipatsenso mwana wina.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
namucha dzina lace Yosefe; ndipo anati, Yehova anandionjezera ine mwana wamwamuna wina.