Genesis 30:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Labani adamuuza kuti, “Undilole kuti ndinenepo mau aŵa, ‘Ine ndi nzeru zamtundu ndadziŵadi kuti Chauta wandidalitsa chifukwa cha iwe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Labani anati kwa iye, Ngatitu ndikapeza ufulu pamaso pako, ukhale, chifukwa ndazindikira kuti Yehova wandidalitsa ine chifukwa cha iwe.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Labani anati kwa iye, “Chonde, ngati mungandikomere mtima musapite chifukwa ndadziwa kudzera mwa kuwombeza kwanga kuti Yehova wandidalitsa chifukwa cha inu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Labani anati kwa iye, Ngatitu ndikapeza ufulu pamaso pako, ukhale, cifukwa ndazindikira kuti Yehova wandidalitsa ine cifukwa ca iwe.