Genesis 30:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adayankha kuti, “Mukudziŵa m'mene ndakugwirirani ntchito, ndi m'mene zoŵeta zanu zaswanirana kwambiri pozisamala ine.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye anati kwa Labani, Udziwa iwe chomwe ndakutumikira iwe ndi chomwe zachita zoweta zako ndi ine.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Yakobo anati kwa iye, “Inu mukudziwa mmene ine ndakugwirirani ntchito ndi mmene ziweto zanu zaswanira pamene ine ndimazisamalira.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anati kwa Labani, Udziwa iwe comwe ndakutumikira iwe ndi comwe zacita zoweta zako ndi ine.