Genesis 30:31 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Apo Labani adamufunsa kuti, “Kodi ndikulipire chiyani?” Yakobe adayankha kuti, “Sindifuna malipiro ena aliwonse. Komabe ndidzapitirira kukuŵeterani zoŵeta zanu, mukavomera kuchita zimene ndinene.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye anati, Ndikupatsa iwe bwanji? Ndipo Yakobo anati, Usandipatse ine kanthu; ukandichitira ine chotero, ine ndidzadyetsanso ndi kusunganso ziweto zako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Labani anafunsa, “Ndikupatse chiyani?” Yakobo anayankha, “Musandipatse kanthu. Koma mungondichitira izi ndipo ndidzapitiriza kusamalira nkhosa zanu ndi kuziyangʼanira:
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anati, Ndikupatsa iwe bwanji? Ndipo Yakobo anati, Usandipatse ine kanthu; ukandicitira ine cotero, ine ndidzadyetsanso ndi kusunganso ziweto zako.