Genesis 30:42 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Choncho zoŵeta zikakhala zofooka zinali za Labani, koma zamphamvu zinali za Yakobe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Koma pamene ziweto zinali zofooka, sanaziike zimenezo: ndipo zofooka, zinali za Labani, ndi zolimba zinali za Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma sankayika nthambizo pamene ziweto zofowoka zazikazi zinkakweredwa pakumwa madzi. Choncho ziweto zofowoka zonse zinakhala za Labani, ndi ziweto zamphamvu zinakhala za Yakobo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Koma pamene ziweto zinali zofoka, sanaziika zimenezo: ndipo zofoka zinali za Labani, ndi zolimba zinali za Yakobo.