Genesis 30:43 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mwa njira imeneyi Yakobe adalemera kwambiri. Adakhala ndi zoŵeta zambiri, akapolo aamuna ndi aakazi, ngamira ndi abulu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Munthuyo ndipo analemera kwambiri, nali nazo zoweta zambiri, ndi akapolo aamuna ndi aakazi, ndi ngamira, ndi abulu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mwa njira imeneyi, Yakobo analemera kwambiri ndipo anali ndi ziweto zochuluka kwambiri, antchito aakazi ndi aamuna, ngamira ndi abulu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Munthuyo ndipo anakula kwambiri, nali nazo zoweta zambiri, ndi akapolo amuna ndi akazi, ndi ngamila, ndi aburu.