Genesis 30:7 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Biliha mdzakazi wa Rakele adatenganso pathupi namubaliranso Yakobe mwana wamwamuna.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Biliha mdzakazi wake wa Rakele anatenganso pakati, nambalira Yakobo mwana wamwamuna wachiwiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Biliha, wantchito wa Rakele, anatenganso pathupi nabalira Yakobo mwana wa mwamuna wachiwiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Biliha mdzakazi wace wa Rakele anatenganso pakati, nambalira Yakobo mwana wamwamuna waciwiri.

Recommended Reading