Genesis 30:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Leya ataona kuti waleka kubala, adapereka mdzakazi wake Zilipa kwa Yakobe.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Pamene Leya anaona kuti analeka kubala, anatenga Zilipa mdzakazi wake, nampatsa iye kwa Yakobo kuti akhale mkazi wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Leya anaona kuti waleka kubereka ana, iye anatenga wantchito wake Zilipa namupereka kwa Yakobo kuti alowane naye.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Pamene Leya anaona kuti analeka kubala, anatenga Zilipa mdzakazi wace, nampatsa iye kwa Yakobo kuti akhale mkazi wace.