Genesis 31:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Rakele ndi Leya adayankha kuti, “Palibe chomwe chatitsalira ife kwa bambo wathu choti chikhale choloŵa chathu.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Rakele ndi Leya anayankha, nati kwa iye, Kodi tili nalonso gawo kapena cholowa m'nyumba ya atate wathu?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Rakele ndi Leya anayankha, “Kodi ngati ife tilinso ndi gawo ngati cholowa pa chuma cha abambo athu?
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Rakele ndi Leya anayankha, nati kwa iye, Kodi tiri nalonso gawo kapena colowa m'nyumba ya atate wathu?