Genesis 31:15 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ife bambo wathu akutiyesa alendo. Adatigulitsa, ndipo ndalama zomwe adazipezera pa ifezo, adamwaza zonse.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Kodi satiyesa ife alendo? Chifukwa anatigulitsa ife, nathanso kuononga ndalama zathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kodi abambo athu samationa ife ngati alendo? Iwo anatigulitsa ndi kuwononga ndalama zonse anazipeza pa ifezo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Kodi satiyesa ife alendo? cifukwa anatigulitsa ife, nathanso kuononga ndalama zathu.