Genesis 31:16 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chuma chonse chimene Mulungu wachotsa kwa bambo wathu, ndi chathu ndi cha ana athu. Chitani zimene Mulungu wakuuzani.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Chifukwa kuti chuma chonse Mulungu anachichotsa kwa atate wathu ndi chathu ndi cha ana athu; tsono, zonse wakunenera iwe Mulungu, uchite.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chuma chonse chimene Mulungu walanda abambo athu, ndi chathu ndi ana athu. Tsono inu chitani zimene Mulungu wakuwuzani.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Cifukwa kuti cuma conse Mulungu anacicotsa kwa atate wathu ndi cathu ndi ca ana athu; tsono, zonse wakunenera iwe Mulungu, ucite.