Genesis 31:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Yakobe adakonzekera kuti achoke, kubwerera kwa bambo wake ku dziko la Kanani. Tsono ana ake onse pamodzi ndi akazi ake omwe adaŵakweza pa ngamira.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anauka Yakobo nakweza ana ake ndi akazi ake pa ngamira;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo Yakobo anakonzeka nakweza ana ake ndi akazi ake pa ngamira,
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anauka Yakobo nakweza ana ace ndi akazi ace pa ngamila;