Genesis 31:19 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Labani anali atapita kokameta nkhosa. Ndipo akadali komweko, Rakele adaba timilungu ta m'nyumba mwa Labani, bambo wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Labani ananka kukasenga nkhosa zake: ndipo Rakele anaba aterafi a atate wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Labani atachoka pa khomo kupita kukameta nkhosa, mʼmbuyomu Rakele anaba timafano ta milungu ta abambo ake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Labani ananka kukasenga nkhosa zace: ndipo Rakele anaba aterafi a atate wace.