Genesis 31:2 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adazindikiranso kuti Labani sankamuwonetsa nkhope yabwino ngati kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anaona nkhope ya Labani, taonani, siinamuonekera iye monga kale.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Yakobo anaona kuti Labani sankamuonetsanso nkhope yabwino monga kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo anaona nkhope ya Labani, taonani, siinamuonekera iye monga kale.