Genesis 31:20 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Motero Yakobe adampusitsa Labani Mwaramu uja posamuuza kuti akuchoka.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anathawa kwa Labani Mwaramu mobisika, m'mene sanamuuze iye kuti analinkuthawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komanso nthawi iyi nʼkuti Yakobo atamunamiza Labani Mwaramu posamuwuza zoona kuti afuna kuthawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo anathawa kwa Labani Msuriyamobisika, m'mene sanamuuzeiye kuti analinkuthawa.