Genesis 31:22 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Patapita masiku atatu, Labani adamva kuti Yakobe adathaŵa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsiku lachitatu anamuuza Labani kuti Yakobo wathawa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Patapita masiku atatu, Labani anawuzidwa kuti Yakobo wathawa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsiku lacitatu anamuuza Labani kuti Yakobo wathawa.