Genesis 31:23 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adatenga anthu ake, nkulondola Yakobeyo masiku asanu ndi aŵiri, mpaka adakampezera ku dziko lamapiri la Giliyadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo iye anatenga abale ake pamodzi naye, namlondola iye ulendo wa masiku asanu ndi awiri: nampeza iye paphiri la Giliyadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pomwepo anatengana ndi abale ake namulondola Yakobo kwa masiku asanu ndi awiri ndipo anakamupezera ku Giliyadi, dziko la mapiri.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo iye anatenga abale ace pamodzi naye, namlondola iye ulendo wa masiku asanu ndi awiri: nampeza iye pa phiri la Gileadi.