Genesis 31:24 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Labani Mwaramu uja adalota maloto usiku womwewo. Mulungu adadza namuuza kuti, “Usamuwopseze Yakobe mwa njira iliyonse.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Mulungu anadza kwa Labani Mwaramu usiku, nati kwa iye, Tadziyang'anira wekha, usanene kwa Yakobo kapena zabwino kapena zoipa.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Mulungu anabwera kwa Labani, Mwaramu kutulo usiku nati kwa iye, “Samala kuti usamuopseze Yakobo mwa njira iliyonse.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Mulungu anadza kwa Labani Msuriya usiku, nati kwa iye, Tadziyang'anira wekha, usanene kwa Yakobo kapena zabwino kapena zoipa,