Genesis 31:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Labani adampeza Yakobe atamanga mahema kumapiriko. Nayenso Labaniyo adamanga mahema ake komweko ku dziko lamapiri la Giliyadi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Labani anakomana naye Yakobo. Ndipo Yakobo anamanga hema wake m'phirimo: ndipo Labani ndi abale ake anamanga m'phiri la Giliyadi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamene Labani amamupeza Yakobo, nʼkuti Yakobo atamanga matenti ake ku mapiri a dziko la Giliyadi. Nayenso Labani ndi abale ake anamanga matenti awo komweko.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Labani anakomana naye Yakobo. Ndipo Yakobo anamanga hema wace m'phirimo: ndipo Labani ndi abale ace anamanga m'phiri la Gileadi.