Genesis 31:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chifukwa chiyani wandinyenga ndi kundizemba osandiwuza? Ukadandiwuza, bwenzi nditakulola mokondwa, ndipo bwenzi pali kumaimba nyimbo ndi ting'oma ndi azeze.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Wathawanji iwe mobisika, ndi kundichokera kuseri, osandiuza ine, kuti ndikadakumukitsa iwe ndi kusekerera ndi nyimbo ndi lingaka ndi zeze?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Chifukwa chiyani unandinamiza ndi kuthawa mozemba wosandiwuza? Ukanandiwuza, bwezi titatsanzikana mwa chisangalalo ndi kuyimba nyimbo ndi zisekese ndi azeze.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Wathawanji iwe mobisika, ndi kundicokera kutseri, osandiuza ine, kuti ndikadakumukitsa iwe ndi kusekerera ndi nyimbo ndi lingaka ndi zeze?