Genesis 31:30 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndikudziŵa kuti udachoka chifukwa unkafunitsitsa kubwerera kwanu. Koma bwanji wandibera timilungu tanga?”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Tsono ungakhale ukadamuka chifukwa mtima wako ulinkukhumba nyumba ya atate wako, bwanji waba iwe milungu yanga?
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ndikudziwa kuti unachoka chifukwa unapukwa kufuna kubwerera kwanu kwa abambo ako. Koma nʼchifukwa chiyani unaba milungu yanga?”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Tsono ungakhale ukadamuka cifukwa mtima wako ulinkukhumba nyumba ya atate wako, bwanji waba iwe milungu yanga?