Genesis 31:4 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yakobe adatumiza mau kwa Rakele ndi kwa Leya kuti akakumane naye kubusa kumene kunali zoŵeta zake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anatumiza naitana Rakele ndi Leya adze kubusa ku zoweta zake,
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho Yakobo anatumiza mawu kukayitana Rakele ndi Leya kuti abwere ku busa kumene ankaweta ziweto zake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo anatumiza naitana Rakele ndi Leya adze kubusa ku zoweta zace,