Genesis 31:47 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono muluwo Labani adautcha Yagara-Sahaduta, koma mulu womwewo Yakobe adautcha Galedi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Labani anatcha pamenepo Yegara-Sahaduta; koma Yakobo anatcha Galedi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Labani anawutcha muluwo Yegara-sahaduta, ndipo Yakobo anawutcha Galeeda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Labani anacha pamenepo Yegara-sahaduta; koma Yakobo anacha Galeeda.