Genesis 31:49 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Labani adanenanso kuti, “Chauta atiyang'anire ife tonse aŵiri pamene tikulekana. Motero malowo adaŵatcha Mizipa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndi Mizipa, chifukwa kuti anati, Yehova ayang'anire pakati pa ine ndi iwe, pamene tisiyana wina ndi mnzake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Unatchedwanso Mizipa, chifukwa iye anati, “Yehova aonetsetsa kuti palibe mmodzi mwa ife adzaswe panganoli ngakhale titatalikirana.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndi Mizipa, cifukwa kuti anati, Yehova ayang'anire pakati pa ine ndi iwe, pamene tisiyana wina ndi mnzace.