Genesis 31:50 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Labani adapitirira kunena kuti, Ukamakaŵazunza ana angaŵa, kapena ukakakwatira akazi ena, ngakhale palibe wina ali nafe pano, ukumbukire kuti Mulungu ndiye mboni pakati pa ine ndi iwe.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ukasautsa ana anga akazi, kapena ukatenga akazi kuonjezera pa ana anga, palibe munthu mmodzi ali nafe; taonani, Mulungu ndiye mboni yanga ndi yako.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ngati ukazunza ana anga kapena kukwatira akazi enanso, ngakhale kuti palibe wina amene ali nafe pano, koma kumbukira kuti Mulungu ndiye mboni pakati pathu.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ukasautsa ana anga akazi, kapena ukatenga akazi kuonjezera pa ana anga, palibe munthu mmodzi ali nafe; taonani, Mulungu ndiye mboni yanga ndi yako.