Genesis 31:51 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Labani adauza Yakobe kuti, “Pano pali miyala imene ndaunjika pakati pathu, ndipo pompano pali mwala wachikumbutso.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Labani anati kwa Yakobo. Taona muluwu, taona choimiritsachi, ndachiimiritsa pakati pathu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Labani anatinso kwa Yakobo, “Taona pano pali miyala ndi chipilala chimene ndayimika pakati pa iwe ndi ine.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Labani anati kwa Yakobo. Taona muluwu, taona coimiritsaci, ndaciimiritsa pakati pathu.