Genesis 31:53 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Mulungu wa Abrahamu, Mulungu wa Nahori, Mulungu wa atate ao, ndiye adzatiweruze ife aŵiri.” Motero Yakobe adalumbira m'dzina la Mulungu amene Isaki bambo wake ankamuwopa.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mulungu wa Abrahamu ndi Mulungu wa Nahori, Mulungu wa atate wao aweruze pa ife. Ndipo Yakobo analumbirira pa Kuopsa kwa atate wake Isaki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Mulungu wa Abrahamu ndi Mulungu wa Nahori ndiye adzatiweruze.” Choncho Yakobo analumbira mʼdzina la Mulungu amene Isake, abambo ake ankamuopa.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mulungu wa Abrahamu ndi Mulungu wa Nahori, Mulungu wa atate wao aweruze pa ife. Ndipo Yakobo analumbirira pa Kuopsa kwa atate wace Isake.