Genesis 33:14 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Chonde mbuyanga, tsogolaniko, ine ndiziyenda pang'onopang'ono pambuyo pa zoŵeta ndi ana anga, mpaka ndikakupezani ku Seiri.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Mbuyanga atsogoleretu kapolo wake, ndipo ine ndidzazitsogolera pang'onopang'ono monga mwa mayendedwe a zoweta zili pamaso panga, ndi monga mwa mayendedwe a ana, mpaka ndifike kwa mbuyanga ku Seiri.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Choncho, mbuye wanga lolani kuti mutsogole. Ine ndiziyenda pangʼonopangʼono pambuyo pa ziwetozi ndi anawa mpaka ndikafika ku Seiri.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Mbuyanga atsogoleretu kapolo wace, ndipo ine ndidzazitsogolera pango'no-pang'ono monga mwa mayendedwe a zoweta ziri pamaso panga, ndi monga mwa mayendedwe a ana, mpaka ndifike kwa mbuyanga ku Seiri.