Genesis 33:17 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Yakobe adapita ku Sukoti, ndipo adamangako nyumba yake, pamodzi ndi makola a zoŵeta zake. Nchifukwa chake malowo adatchedwa Sukoti.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anankabe ulendo wake ku Sukoti, namanga nyumba yake pamenepo, namanga makola a zoweta zake: chifukwa chake dzina lake la kumeneko ndi Sukoti.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Komabe Yakobo anapita ku Sukoti. Kumeneko anamanga nyumba yake ndi makola a ziweto zake. Nʼchifukwa chake malowa amatchedwa Sukoti.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo anankabe ulendo wace ku Sukoti, namanga nyumba yace pamenepo, namanga makola a zoweta zace: cifukwa cace dzina lace la kumeneko ndi Sukoti.