Genesis 33:19 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malo amenewo adagula kwa zidzukulu za Hamori, bambo wake wa Sekemu, pa mtengo wa ndalama 100 zasiliva.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anagula ndi ndalama zana limodzi dera la munda kumeneko anamanga hema wake, pa dzanja la ana ake a Hamori atate wake wa Sekemu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Malo amenewo anagula kwa zidzukulu za Hamori, abambo a Sekemu ndi ndalama 100 zasiliva.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anagula ndi ndalama zana limodzi dera la munda kumeneko anamanga bema wace, pa dzanja la ana ace a Hamori atate wace wa Sekemu.