Genesis 33:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono adzakazi aja adadza pamodzi ndi ana ao, nagwada pansi.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo adzakazi anayandikira ndi ana ao, nawerama pansi.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Tsono antchito aja anayandikira naweramitsa mitu pansi.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo adzakazi anayandikira ndi ana ao, nawerama pansi.