Genesis 33:9 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Koma Esau adati, “Mbale wanga, zoŵeta zotere ndili nazo zambiri. Uli nazozi zikhale zako.”
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Esau anati, Zanga zindifikira; mbale wanga, khala nazo zako iwe wekha.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Koma Esau anati, “Mʼbale wanga, ine ndili nazo kale zambiri. Zinthu zakozi sunga.”
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Esau anati, Zanga zindifikira; mbale wanga, khala nazo zako iwe wekha.