Genesis 35:14 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adaimika chimwala chachikumbutso pa malo amenewo. Adapereka chopereka cha chakumwa pamwalapo, nathirapo mafuta.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anaimiritsa mwala pamalo pamene ananena ndi iye, choimiritsa chamwala: ndipo anathira pamenepo nsembe yothira, nathirapo mafuta.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anayika mwala wachikumbutso pa malo pamene Mulungu anayankhula naye paja. Iye anathirapo nsembe yachakumwa ndi yamafuta.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakoboanaimiritsamwala pamalo pamene ananena ndi iye, coimiritsa camwala: ndipo anathira pamenepo nsembe yothira, nathirapo mafuta.