Genesis 35:15 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Malo amene Mulungu adalankhula naye, Yakobe adaŵatcha Betele.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anatcha dzina lake la pamalo pamene Mulungu ananena ndi iye, Betele.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anawatcha malo amene Mulungu anayankhula naye aja kuti Beteli.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anacha dzina lace la pamalo pamene Mulungu ananena ndi iye, Beteli.