Genesis 35:25 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Biliha mdzakazi wa Rakele anali aŵa: Dani ndi Nafutali.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ana amuna a Biliha mdzakazi wake wa Rakele: ndiwo Dani ndi Nafutali;
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Biliha, wantchito wa Rakele ndi awa: Dani ndi Nafutali.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ana amuna a Biliha mdzakazi wace wa Rakele: ndiwo Dani ndi Nafitali;