Genesis 35:26 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ana a Zilipa mdzakazi wa Leya anali aŵa: Gadi ndi Asere. Ameneŵa ndiwo ana a Yakobe amene adabadwira ku Mesopotamiya.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
ndipo ana amuna a Zilipa mdzakazi wake wa Leya: ndiwo Gadi ndi Asere: amenewo ndi ana amuna a Yakobo amene anabala iye m'Padanaramu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Ana a Zilipa wantchito wa Leya ndi awa: Gadi ndi Aseri. Awa ndiwo ana a Yakobo amene anabadwira ku Padanaramu.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
ndipo ana amuna a Zilipa mdzakazi wace wa Leya: ndiwo Gadi ndi Aseri: amenewo ndi ana amuna a Yakobo amene anabala iye m'Padanaramu.