Genesis 35:27 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Yakobe adakafika kwa bambo wake Isaki ku Mamure (kumenenso kunkatchedwa ku Kiriyati-Ariba kapena Hebroni), kumene Abrahamu ndi Isaki ankakhala kale.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anafika kwa Isaki atate wake ku Mamure, ku Kiriyati-Ariba (ndiwo Hebroni) kumene anakhala Abrahamu ndi Isaki.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo anafika ku mudzi kwa abambo ake Isake ku Mamre, (kumene kunkatchedwa ku Kiriyati-Ariba kapenanso Hebroni) kumene Abrahamu ndi Isake anakhalako kale.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo anafika kwa Isake atate wace ku Mamre, ku KiriyatiAriba (ndiwo Hebroni) kumene anakhala Abrahamu ndi Isake.