Genesis 35:28 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Isaki adamwalira ali wa zaka 180.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo masiku a Isaki anali zaka zana limodzi kudza makumi asanu ndi atatu.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Isake anakhala ndi moyo zaka 180.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo masiku a Isake anali zaka zana limodzi kudza makumi asanu ndi atatu.