Genesis 35:29 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Ndipo adafa ndi kuikidwa m'manda, ali nkhalamba zedi. Ana ake, Esau ndi a Yakobe ndiwo adamuika m'manda.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Isaki anatsirizika nafa, nasonkhanitsidwa kwa anthu a mtundu wake, wokalamba ndi wa masiku okwanira: ndipo Esau ndi Yakobo ana ake amuna anamuika iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Anamwalira ali wokalamba kwambiri ndipo anakakhala ndi anthu a mtundu wake. Ndipo ana ake Esau ndi Yakobo anamuyika mʼmanda.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Isake anatsirizika nafa, nasonkhanitsidwa kwa anthu a mtundu wace, wokalamba ndi wa masiku okwanira: ndipo Esau ndi Yakobo ana ace amuna anamuika iye.