Genesis 35:5 — Compare Translations

4 translations compared side by side

Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Pamene Yakobe ndi ana ake adachoka, anthu onse a mizinda yozungulira adachita mantha, motero sadaŵatsatire.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anapita ndipo kuopsa kwa Mulungu kudagwera midzi yakuwazinga, ndipo sanalondole ana a Yakobo.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Pamenepo ananyamuka, ndipo mtima woopa Mulungu unagwera anthu onse a mʼmizinda yozungulira, kotero kuti palibe aliyense amene anatsatira banja la Yakobo.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anapita, ndipo kuopsa kwa Mulungu kudagwera midzi yakuwazinga, ndipo sanalondola ana a Yakobo.