Genesis 35:6 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Tsono Yakobe adafika ndi anthu ake ku Luzi (ndiye kuti Betele) m'dziko la Kanani.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo Yakobo anafika ku Luzi, ndiko ku dziko la Kanani (ndiwo Betele), iye ndi anthu onse anali pamodzi ndi iye.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Yakobo ndi anthu onse anali naye aja anafika ku Luzi (ku Beteli) mu dziko la Kanaani.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo Yakobo anafika ku Luzi, ndiko ku dziko la Kanani (ndiwo Beteli), iye ndi anthu onse anali pamodzi ndi iye.