Genesis 35:7 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Adamanga guwa kumeneko, ndipo malowo adaŵatcha Betele, chifukwa kumeneko nkumene Mulungu adadziwulula kwa Yakobe pamene ankathaŵa mbale wake.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
Ndipo anamanga kumeneko guwa la nsembe, natcha pamenepo El Betele: pakuti kumeneko Mulungu anaonekera kwa iye muja anathawa pa nkhope ya mbale wake.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Kumeneko anamanga guwa lansembe nalitcha Eli Beteli, chifukwa kunali kumeneko kumene Mulungu anadziwulula yekha kwa Yakobo pamene ankathawa mʼbale wake.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
Ndipo anamanga kumeneko guwa la nsembe, Dacha pamenepo El Beteli: pakuti kumeneko Mulungu anaonekera kwa iye muja anathawa pa nkhope ya mbale wace.