Genesis 36:10 — Compare Translations
4 translations compared side by side
Chewa (Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa)
Maina a ana aamuna a Esau naŵa: Elifazi mwana wa Ada mkazi wa Esau, ndi Reuele mwana wa Basemati mkazi wa Esau.
Chewa 1922 (Buku Lopatulika)
amenewa ndi maina a ana amuna a Esau: Elifazi mwana wamwamuna wa Ada, mkazi wake wa Esau, Reuwele mwana wamwamuna wa Basemati mkazi wake wa Esau.
Chewa 2002 (Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero)
Awa ndi mayina a ana aamuna a Esau: Elifazi, mwana wa Ada, mkazi wa Esau, ndi Reueli, mwana wamwamuna wa Basemati, mkazi wa Esau.
Chewa Bible (BL) 1992 - Buku Lopatulika
amenewa ndi maina a ana amuna a Esau: Elifazi mwana wamwamuna wa Ada, mkazi wace wa Esau, Reueli mwana wamwamuna wa Basemati mkazi wace wa Esau.